Tomorrow am either buying a new car or am graduating. One thing must happen whether rain or sunshine.
Fairly used and in a very good working condition. Tiguleni tigule bundle tizilowa pa X mix shombokizo manyizo. Komanso tilipira rent. K1,700,000
Join us on this coming Saturday (22nd August) at BYC. Bwerani tizajoge pa bill ya MASM. Inu zabwino ayi?
Anthu aku Dowa muli ndi ndi nsanje yochititsa manyazi😏. Mzanu wadutsitsa bwinobwino chomupangira report ncha? Muzipanga nsanje moopa Mulungu.





















