Akometsi (@akometsimw) header
Akometsi (@akometsimw) profile picture

We promote brands, entertain people and exaggerate issues. No sad moments here.

Malawi
Joined January 2020
Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)
FULL-TIME ⚽️ Chelsea 2-0 Man U
1
269
GOAAAAALLLLL ⚽️ Chelsea 2-0 Man Pa 64 minutes
153
Chelsea Disallowed goal pa 15 Minutes, Man U Disallowed goal pa 35 minutes. kwachemeratu 🙌🏾
1
342
Koma anthu ndalama zomagawira ma Followers awo akuzitenga kuti ? 🙌🏾 Uyu, akupitirizabe kugawa ndalama , ma K100,000 ndima Bundle kwa anthu omwe amupanga follow 🙌🏾 Kumupangeni follow, nkukatengakoso ndalama zanu. Zosadabwitsa aku user iPhone 18
103
Akuti anakula movutika moti Ku school ankatenga Mowa Chifukwa chosowa Juice!!😸 🧘🏿‍♂️
259
Mwaiona bwanji album yatsopano ya Asini 'Khumi 'Wapala ? olo Waiswa ?
104
Pa nkhani yoti sanafunse funsolo, izi ndizomwe wapanga post Mkometsi Kwax ku page kwake. Iye wati: “Nokha munamva za mfuti kumene kuja, ndiye mumati ndifunse ndine? Ineyo John Chilembwe wanu?🙄”
102
Highlights: Sky@10. Umu ndi mmene zinalili pamene mabwana anakumana ku Lilongwe ku launch yama Electric Cars a Sky Energy komwenso amasangalala kuti atha zaka 10.
2
576
Kodi mukuti Mkometsi Kwax sanafunse funso leni leni kwa Namadingo, funso leni leni linali loti chani?
303
Men only: Kodi chomwe chimakunyasani pa akazi ndi chani ?
197
Sir Patrick Stewart was deceived by his mother to believe that he was circumcised, only to know the truth at 76 when his wife said he wasn't circumcised. Bizarre right?
1
4
627
Sky@10: Ku BICC kuno amene sanatchene ndi Bensam yekha eeh anthu awusosola ulusi🔥🔥🔥 Kodi inu sanakuyitaneni?
12
1,573
Kuno nde anachita kumuuza kuti nyangwita zako umavala zija kunoko ayi ndipo Kell Kay wamvera. Muombeleni mmanja mwamuna wa Tamanda watchena 👏🏾 Sky@10
8
1,619
Koma Gwamba watchena 👏🏼👏🏼 Zikuchitika ku BICC komwe Sky Energy ikukondwelera zaka 10. Tayamikirani watchena uyu.
1
14
1,912
Sky@10: Sitikudziwa kuti ndi chani kweni kweni koma kuno ku BICC kukuchitika zinthu zomwe nafenso zatipatsa chidwi. Yathu ija, tikhalanso pompano kuwatapa mkamwa, kupeza ma mistake komanso kukokomeza zomwe zizichitikazo. Tava kununkhila zakudya ndi zakumwa. Achina Gwamba, Namadingo, Teddy Makadi, Praise Umali, Kell Kay akhalanso pompano akuti.
4
799
Zayambika ndipo kwachemaratu 🔥🔥🔥🙌🏾 Sopano Zeze watulutsa list yoyamba ya oimba 4, omwe akapange nawo perform ku Concert yake 'Tigona Panja' 🔥 Wayamba ndi Crispy Malawi, Driemo, Lady Aika ndi Skeffa Chimoto 🔥 Ndiye paja ma ticket ayambira K10,000. Ndipo ma ticket awawa akutha mawa kwinako adhula, guliranitu nthawi yabwino. Linkie 🔥
2
7
65
2,774
KODI MUMADZIWA ? Zeze yemwe waonekera kwambiri as Amapiano Artist kwa zaka 4 zimenezi komano watulutsa kale ma hit songs okwana 50 ? Just imagine🙌🏾 Zeze's Top 50 songs 1. Ndilira Mumvula ft. Yo Maps, HarryCane & Leumas 2. Kusangalala (Acoustic version) 3. Achisale ft. LeuMas, Nae Rae 4. Alamu Anu ft. NyasaPiano 5. Vula Malaya ft. Malimba Music, Leumas 6. Zonsezi Ndi Zeze 7. Mavuto ft. XDuppy, LeuMas 8. Chule ft. Afana Ceez, Tuno, Leumas, Vj Ice 9. Ndathela Pano 10. Maluzi ft. LeuMas, Amfumu Collins Bandawe 11. Mphaka ft. LeuMas, Achina Ghatta Ase, Richard Billy & Dj Drew 12. Mbama ft. LeuMas 13. Mvetsela ft. Temwah 14. Zalowa ft. Leumas, Yanos Central 15. Ndavomela ft. Don Bunji 16. Taima ft. Leumas 17. Lero ft. The Daredevilz 18. Ndamva 19. Kagwele Uko ft. Leumas, Hayz Emgola 20. Ukuzatani? ft. Leumas, Imnotsteelo, Koollay 21. Zowawa ft. Leumas 22. HEY YOU SIBUSISO ft. Dj Maphorisa, Vulela 2, Myztro, Mlusician, Debow Taliana 23. Ndamutuluka ft. LeuMas 24. Lero Zogona ayi ft. Leumas 25. Yemweyo ft. LeuMas, Zani Challe 26. Please Don't Judge Me 27. Thupi Lako ft. LeuMas, Hayze Engola 28. Azandikanganila ft. Leumas 29. Thank You ft. Leumas, VJ Ice & Dj Drew 30. Vuto Ndichani ft. Temwah 31. Sindimazitengela ft. LeuMas 32. Tipalamulapo Pano ft. LeuMas 33. Njoka 34. Asandidutse ft. LeuMas 35. Mkazi Mbambande ft. Leumas 36. Mowa Wadzulo ft. Leumas, Black Don & Siirprincey 37. 6-2-6 ft. Temwah 38. Ndabalalika ft. Vj Ice 39. Monday to Sunday ft. Leumas 40. Kale ft. Temwah 41. Ndasangalala with Way2Savage, Joe ikon 42. Ku mowa with Charisma 43. Anzanu with Kineo, Aidfest Madness 44. Chete with Malinga Mafia 45. Simmene kuliri with Deo Cruger 46. Ma set with Jain Cactus, Leumas, Durk 47. Limodzi with Joe ikon 48. Kadigong with Sho Madjozi, Tiwa Savage 49. Feli with Naerae & Leumas 50. Kwayipa with Fada Moti Kuti muonetsetse nyimbo zonsezi Ghetto imazidziwa, ndipo imaimba nawo palipose. Pakuti nyimbo zake imazikonda kwambiri ndi Ghetto, ndichifukwa chakeso waiganizira Ghetto yo, ndipo ticket yake yayambira 10K 👏🏾 Ndiye ngati kuma show aanthu ena amaimba mpakana mbembembe, ndiye ku concert yakeyi 'Tigona Panja' akaimba nyimbo 50 zonsezi ikatha liti ? Yangoyeneradi, kukayamba pa 31 Zezember mpakana 2027 iyi coz no ! Zeze yu anadza 🔥 Tiyeni ukuku tikasangalale, ma ticket a 10K akutha mawa, zungufunika kuguliratu 🔥👏🏾
2
2
25
2,538
Chikayamba kumene umaona ngt vuto ndamene anasiyana nayeyo 😂🙌 🔨
1
2
419
Bwanji inuyo muli ndi phone number ya Ex wanu ?
1
744